Nehemiya 7:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Atsogoleri ena a nyumba za makolo anapereka zinthu zothandizira pa ntchito.+ Bwanamkubwa* anapereka kumalo osungira chuma ndalama za dalakima* zagolide 1,000, mbale zolowa 50 ndi mikanjo ya ansembe 530.+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:70 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2142
70 Atsogoleri ena a nyumba za makolo anapereka zinthu zothandizira pa ntchito.+ Bwanamkubwa* anapereka kumalo osungira chuma ndalama za dalakima* zagolide 1,000, mbale zolowa 50 ndi mikanjo ya ansembe 530.+