Nehemiya 7:70 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 70 Ndiye panali atsogoleri+ ena a nyumba za makolo+ amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchito.+ Tirisata+ anapereka ndalama za dalakima* zagolide 1,000, mbale zikuluzikulu 50, ndi mikanjo ya ansembe 530 kumalo osungira chuma.+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:70 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2142
70 Ndiye panali atsogoleri+ ena a nyumba za makolo+ amene anapereka mphatso zothandizira pa ntchito.+ Tirisata+ anapereka ndalama za dalakima* zagolide 1,000, mbale zikuluzikulu 50, ndi mikanjo ya ansembe 530 kumalo osungira chuma.+