Ezara 2:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Pa chifukwa chimenechi, Tirisata*+ anawauza kuti sayenera kudya+ zinthu zopatulika koposa, kufikira patakhala wansembe wokhala ndi Urimu+ ndi Tumimu. Nehemiya 7:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pa chifukwa chimenechi, Tirisata*+ anawauza kuti sayenera kudya+ zinthu zopatulika koposa kufikira patakhala wansembe wokhala ndi Urimu+ ndi Tumimu.+
63 Pa chifukwa chimenechi, Tirisata*+ anawauza kuti sayenera kudya+ zinthu zopatulika koposa, kufikira patakhala wansembe wokhala ndi Urimu+ ndi Tumimu.
65 Pa chifukwa chimenechi, Tirisata*+ anawauza kuti sayenera kudya+ zinthu zopatulika koposa kufikira patakhala wansembe wokhala ndi Urimu+ ndi Tumimu.+