Levitiko 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anamuveka chovala cha pachifuwa+ ndi kuika Urimu ndi Tumimu+ m’chovala cha pachifuwacho. Deuteronomo 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo kwa Levi anati:+“Tumimu ndi Urimu+ wanu ndizo za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a Meriba.+
8 Ndipo kwa Levi anati:+“Tumimu ndi Urimu+ wanu ndizo za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a Meriba.+