Levitiko 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anamuveka chovala chapachifuwa+ nʼkuika Urimu ndi Tumimu+ mʼchovala chapachifuwacho.