Levitiko 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo zotsala za nsembe yambewu ndi za Aroni ndi ana ake, popeza ndi zopatulika koposa zochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.+ Levitiko 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Lamulo la nsembe ya kupalamula+ lili motere: Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+
10 Ndipo zotsala za nsembe yambewu ndi za Aroni ndi ana ake, popeza ndi zopatulika koposa zochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova.+