Salimo 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+ Yesaya 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye ndi amene adzakhale pamalo apamwamba.+ Malo ake okhala adzakhala otetezeka m’matanthwe movuta kufikamo.+ Iye adzapatsidwa chakudya+ ndipo madzi ake sadzatha.”+ Mateyu 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+ 1 Timoteyo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti kuchita masewera olimbitsa thupi n’kopindulitsa pang’ono, koma kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ n’kopindulitsa m’zonse,+ chifukwa kumakhudza lonjezo la moyo uno ndi moyo umene ukubwerawo.+
10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+
16 Iye ndi amene adzakhale pamalo apamwamba.+ Malo ake okhala adzakhala otetezeka m’matanthwe movuta kufikamo.+ Iye adzapatsidwa chakudya+ ndipo madzi ake sadzatha.”+
33 “Chotero pitirizani kufunafuna ufumu choyamba ndi chilungamo chake,+ ndipo zina zonsezi zidzawonjezedwa kwa inu.+
8 Pakuti kuchita masewera olimbitsa thupi n’kopindulitsa pang’ono, koma kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ n’kopindulitsa m’zonse,+ chifukwa kumakhudza lonjezo la moyo uno ndi moyo umene ukubwerawo.+