Miyambo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mfumu ikamukomera munthu mtima, munthuyo amakhala ndi moyo wabwino.Kukoma mtima kwake kuli ngati mtambo wa mvula mʼnyengo ya chilimwe.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:15 Nsanja ya Olonda,5/15/2007, tsa. 20
15 Mfumu ikamukomera munthu mtima, munthuyo amakhala ndi moyo wabwino.Kukoma mtima kwake kuli ngati mtambo wa mvula mʼnyengo ya chilimwe.+