Salimo 72:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Inu Mulungu, thandizani mfumu kuti iziweruza mogwirizana ndi zigamulo zanu,Ndipo dziwitsani mwana wa mfumu za chilungamo chanu.+ Salimo 72:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzakhala ngati mvula imene imagwera pa udzu umene watchetchedwa,Ngati mvula yamvumbi imene imanyowetsa nthaka.+
72 Inu Mulungu, thandizani mfumu kuti iziweruza mogwirizana ndi zigamulo zanu,Ndipo dziwitsani mwana wa mfumu za chilungamo chanu.+
6 Adzakhala ngati mvula imene imagwera pa udzu umene watchetchedwa,Ngati mvula yamvumbi imene imanyowetsa nthaka.+