-
1 Mbiri 22:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Tsopano mwana wanga, Yehova akhale nawe ndipo zinthu zikuyendere bwino. Umange nyumba ya Yehova Mulungu wako, mogwirizana ndi zimene iye analankhula zokhudza iweyo.+ 12 Yehova akupatse nzeru ndi kuzindikira.+ Akupatsenso mphamvu zotsogolera Aisiraeli, kuti usunge chilamulo cha Yehova Mulungu wako.+
-