Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Nthambi+ idzaphuka pachitsa cha Jese,+

      Ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzabereka zipatso.

  • Yesaya 53:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Iye adzaphuka ngati nthambi+ pamaso pawinawake* ndiponso ngati muzu wotuluka mʼnthaka youma.

      Saoneka ngati munthu wapadera kapena waulemerero,+

      Ndipo tikamuona, maonekedwe ake si ochititsa chidwi moti ife nʼkukopeka naye.*

  • Yeremiya 33:15, 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 ‘Mʼmasiku amenewo ndiponso nthawi imeneyo ndidzameretsera Davide mphukira+ yolungama* ndipo mphukirayo idzaweruza mwachilungamo mʼdzikoli.+ 16 Mʼmasiku amenewo Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Yerusalemu adzakhala mwamtendere.+ Yerusalemu azidzatchulidwa kuti, Yehova Ndi Chilungamo Chathu.’”+

  • Zekariya 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 ‘Tamvetsera iwe Yoswa mkulu wa ansembe ndi anzako amene akhala pansi kutsogolo kwako, chifukwa amuna amenewa ali ngati chizindikiro. Ine ndibweretsa mtumiki wanga+ dzina lake Mphukira.+

  • Mateyu 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritse mawu amene Mulungu ananena kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena