1 Samueli 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwamuna ameneyu dzina lake anali Nabala,+ ndipo mkazi wake anali Abigayeli.+ Mkazi wakeyu anali wanzeru kwambiri+ ndi wokongola, koma mwamunayu anali wouma mtima ndi wokonda kuchita zinthu zoipa.+ Mwamuna ameneyu anali wa m’banja la Kalebe.+ 2 Mbiri 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo anthu osowa chochita+ ndi opanda pake+ anasonkhana kumbali yake. Pamapeto pake iwo anakhala amphamvu kuposa Rehobowamu+ mwana wa Solomo pamene Rehobowamuyo anali wamng’ono komanso wamantha,+ ndipo sanathe kulimbana nawo. Yesaya 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu wakhalidwe loipayo, njira zake n’zoipa.+ Iye amakonza zochita khalidwe lotayirira,+ n’cholinga choti apweteke anthu ozunzika pogwiritsa ntchito mawu abodza,+ ngakhale pamene munthu wosauka akunena zoona.
3 Mwamuna ameneyu dzina lake anali Nabala,+ ndipo mkazi wake anali Abigayeli.+ Mkazi wakeyu anali wanzeru kwambiri+ ndi wokongola, koma mwamunayu anali wouma mtima ndi wokonda kuchita zinthu zoipa.+ Mwamuna ameneyu anali wa m’banja la Kalebe.+
7 Ndipo anthu osowa chochita+ ndi opanda pake+ anasonkhana kumbali yake. Pamapeto pake iwo anakhala amphamvu kuposa Rehobowamu+ mwana wa Solomo pamene Rehobowamuyo anali wamng’ono komanso wamantha,+ ndipo sanathe kulimbana nawo.
7 Munthu wakhalidwe loipayo, njira zake n’zoipa.+ Iye amakonza zochita khalidwe lotayirira,+ n’cholinga choti apweteke anthu ozunzika pogwiritsa ntchito mawu abodza,+ ngakhale pamene munthu wosauka akunena zoona.