1 Samueli 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho mudziwe zimenezi ndi kuona zimene mungachite, chifukwa atsimikiza kudzetsa tsoka+ pa mbuyanga ndi onse a m’nyumba yake, pakuti mbuye wathu ndi munthu wopanda pake,+ sitingathe kulankhula naye.” 1 Samueli 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Davide anali atanena kuti: “Ine ndinalondera zinthu zake m’chipululu ndipo palibe chinthu chake ngakhale chimodzi chimene chinasowa.+ N’zokhumudwitsa kuti munthu ameneyu akundibwezera zoipa pa zabwino zimene ndinam’chitira.+ Yesaya 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wopusa sadzatchedwanso wopatsa, ndipo munthu wopanda khalidwe sadzatchedwa wolemekezeka,+
17 Choncho mudziwe zimenezi ndi kuona zimene mungachite, chifukwa atsimikiza kudzetsa tsoka+ pa mbuyanga ndi onse a m’nyumba yake, pakuti mbuye wathu ndi munthu wopanda pake,+ sitingathe kulankhula naye.”
21 Davide anali atanena kuti: “Ine ndinalondera zinthu zake m’chipululu ndipo palibe chinthu chake ngakhale chimodzi chimene chinasowa.+ N’zokhumudwitsa kuti munthu ameneyu akundibwezera zoipa pa zabwino zimene ndinam’chitira.+