Yesaya 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsoka kwa amene akunena kuti chabwino n’choipa ndipo choipa n’chabwino,+ amene akuika mdima m’malo mwa kuwala ndi kuwala m’malo mwa mdima, amene akuika zowawa m’malo mwa zotsekemera,* ndi zotsekemera m’malo mwa zowawa.+ Malaki 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndithu, anthu inu mudzaonanso kusiyana pakati pa munthu wolungama ndi woipa+ ndiponso pakati pa munthu amene akutumikira Mulungu ndi amene sanatumikirepo Mulungu.”+
20 Tsoka kwa amene akunena kuti chabwino n’choipa ndipo choipa n’chabwino,+ amene akuika mdima m’malo mwa kuwala ndi kuwala m’malo mwa mdima, amene akuika zowawa m’malo mwa zotsekemera,* ndi zotsekemera m’malo mwa zowawa.+
18 Ndithu, anthu inu mudzaonanso kusiyana pakati pa munthu wolungama ndi woipa+ ndiponso pakati pa munthu amene akutumikira Mulungu ndi amene sanatumikirepo Mulungu.”+