Numeri 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wa fuko la Yuda anali Kalebe,+ mwana wa Yefune. Numeri 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi, ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, adzaiona nthakayo chifukwa akhala akumvera Yehova ndi mtima wonse.’
12 Koma Kalebe+ mwana wa Yefune Mkenizi, ndi Yoswa+ mwana wa Nuni, adzaiona nthakayo chifukwa akhala akumvera Yehova ndi mtima wonse.’