Esitere 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Hamani anatenga chovala+ ndi hatchi, ndipo chovalacho anaveka Moredekai.+ Kenako anam’kwezeka pahatchiyo ndi kumuyendetsa m’bwalo+ la mzinda, akufuula pamaso pake kuti:+ “Umu ndi mmene timachitira ndi munthu amene mfumu yafuna kum’patsa ulemu.”+ Luka 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kunjako n’kumene inu mudzalira ndi kukukuta mano,+ pamene mudzaona Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, komanso aneneri onse ali mu ufumu wa Mulungu,+ koma inuyo atakukankhirani kunja.
11 Pamenepo Hamani anatenga chovala+ ndi hatchi, ndipo chovalacho anaveka Moredekai.+ Kenako anam’kwezeka pahatchiyo ndi kumuyendetsa m’bwalo+ la mzinda, akufuula pamaso pake kuti:+ “Umu ndi mmene timachitira ndi munthu amene mfumu yafuna kum’patsa ulemu.”+
28 Kunjako n’kumene inu mudzalira ndi kukukuta mano,+ pamene mudzaona Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, komanso aneneri onse ali mu ufumu wa Mulungu,+ koma inuyo atakukankhirani kunja.