Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 65:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Atumiki anga adzafuula mokondwa chifukwa chokhala ndi chimwemwe mumtima,+ koma inuyo mudzalira chifukwa chopwetekedwa mtima ndipo mudzafuula chifukwa chosweka mtima.+

  • Mateyu 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 pamene ana a ufumuwo+ adzaponyedwa kunja kumdima. Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.”+

  • Mateyu 13:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Kenako adzawaponya m’ng’anjo yamoto.+ Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena