Mateyu 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 pamene ana a ufumuwo+ adzaponyedwa kunja kumdima. Kumeneko adzalira ndi kukukuta mano.”+ Mateyu 24:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamenepo adzam’patsa chilango choopsa+ ndipo adzam’ponya kumene kuli anthu onyenga. Kumeneko ndiye kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.+ Luka 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kunjako n’kumene inu mudzalira ndi kukukuta mano,+ pamene mudzaona Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, komanso aneneri onse ali mu ufumu wa Mulungu,+ koma inuyo atakukankhirani kunja.
51 Pamenepo adzam’patsa chilango choopsa+ ndipo adzam’ponya kumene kuli anthu onyenga. Kumeneko ndiye kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.+
28 Kunjako n’kumene inu mudzalira ndi kukukuta mano,+ pamene mudzaona Abulahamu, Isaki ndi Yakobo, komanso aneneri onse ali mu ufumu wa Mulungu,+ koma inuyo atakukankhirani kunja.