Mateyu 24:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Choncho adzamupatsa chilango choopsa ndipo adzamuponya kumene kuli anthu achinyengo. Kumeneko iye adzalira komanso kukukuta mano.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:51 Nsanja ya Olonda,3/1/2004, tsa. 13
51 Choncho adzamupatsa chilango choopsa ndipo adzamuponya kumene kuli anthu achinyengo. Kumeneko iye adzalira komanso kukukuta mano.”+