Mateyu 24:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamenepo adzam’patsa chilango choopsa+ ndipo adzam’ponya kumene kuli anthu onyenga. Kumeneko ndiye kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:51 Nsanja ya Olonda,3/1/2004, tsa. 13
51 Pamenepo adzam’patsa chilango choopsa+ ndipo adzam’ponya kumene kuli anthu onyenga. Kumeneko ndiye kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.+