Miyambo 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zoyembekezera za olungama zimasangalatsa,+ koma chiyembekezo cha oipa chidzawonongeka.+ Miyambo 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu woipa akafa, chiyembekezo chake chimawonongeka,+ ndipo zimene anali kuyembekezera kuchokera ku mphamvu zake sizichitika.+
7 Munthu woipa akafa, chiyembekezo chake chimawonongeka,+ ndipo zimene anali kuyembekezera kuchokera ku mphamvu zake sizichitika.+