Salimo 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho moyo wanga ukukondwera, ndipo ndidzakhala wosangalala.+Komanso ndidzakhala wotetezeka.+ Aroma 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwa ameneyunso, ndiponso chifukwa cha chikhulupiriro, takhala ndi ufulu wolowa+ m’kukoma mtima kwakukulu, mmene tilimo tsopano. Ndipo tiyeni tikondwere chifukwa cha chiyembekezo+ cha ulemerero wa Mulungu. Aroma 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kondwerani ndi chiyembekezocho.+ Pirirani chisautso.+ Limbikirani kupemphera.+
2 Mwa ameneyunso, ndiponso chifukwa cha chikhulupiriro, takhala ndi ufulu wolowa+ m’kukoma mtima kwakukulu, mmene tilimo tsopano. Ndipo tiyeni tikondwere chifukwa cha chiyembekezo+ cha ulemerero wa Mulungu.