Miyambo 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+ Miyambo 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mkwiyo wa mfumu umatanthauza amithenga a imfa,+ koma munthu wanzeru ndi amene amauziziritsa.+
35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+