Miyambo 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu oipa adzagwadira abwino,+ ndipo oipa adzagwada pazipata za munthu wolungama.