Genesis 42:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano Yosefe ndiye anali wolamulira m’dzikomo.+ Iye ndiye anali kugulitsa tirigu kwa anthu onse ochokera kumayiko ena onse.+ Choncho abale a Yosefe anafika kwa iye. Anamugwadira n’kumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+ Yesaya 60:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli.
6 Tsopano Yosefe ndiye anali wolamulira m’dzikomo.+ Iye ndiye anali kugulitsa tirigu kwa anthu onse ochokera kumayiko ena onse.+ Choncho abale a Yosefe anafika kwa iye. Anamugwadira n’kumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+
14 “Ana a anthu okusautsa adzabwera kwa iwe atawerama.+ Onse amene anali kukuchitira chipongwe adzagwada pamapazi ako,+ ndipo adzakutcha mzinda wa Yehova, Ziyoni+ wa Woyera wa Isiraeli.