Genesis 47:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yosefe anasonkhanitsa ndalama zonse zimene zinali m’dziko la Iguputo ndi la Kanani, zomwe anthu anali kugulira chakudya.+ Iye anali kutenga ndalamazo kuzipititsa kunyumba kwa Farao.
14 Yosefe anasonkhanitsa ndalama zonse zimene zinali m’dziko la Iguputo ndi la Kanani, zomwe anthu anali kugulira chakudya.+ Iye anali kutenga ndalamazo kuzipititsa kunyumba kwa Farao.