Genesis 41:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Njala ija inafalikira padziko lonse lapansi.+ Zitatero, Yosefe anayamba kutsegula nkhokwe zonse zimene zinali pakati pawo n’kuyamba kugulitsa chakudyacho kwa Aiguputo,+ chifukwa njalayo inali itakula kwambiri m’dziko la Iguputo. Genesis 44:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Patapita nthawi bambo athu anatiuza kuti, ‘Mubwerere, mukatigulire chakudya pang’ono.’+
56 Njala ija inafalikira padziko lonse lapansi.+ Zitatero, Yosefe anayamba kutsegula nkhokwe zonse zimene zinali pakati pawo n’kuyamba kugulitsa chakudyacho kwa Aiguputo,+ chifukwa njalayo inali itakula kwambiri m’dziko la Iguputo.