Genesis 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinalota tikumanga mitolo ya tirigu pakati pa munda. Mtolo wanga unadzuka n’kuima chilili. Mitolo yanunso inadzuka, ndipo inazungulira mtolo wanga n’kuyamba kuuweramira.”+ Genesis 37:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsiku linanso analota maloto ena, ndipo anakauza abale akewo kuti: “Leronso ndinalota maloto ena. Ndinalota dzuwa ndi mwezi ndiponso nyenyezi zokwanira 11 zikundigwadira.”+
7 Ndinalota tikumanga mitolo ya tirigu pakati pa munda. Mtolo wanga unadzuka n’kuima chilili. Mitolo yanunso inadzuka, ndipo inazungulira mtolo wanga n’kuyamba kuuweramira.”+
9 Tsiku linanso analota maloto ena, ndipo anakauza abale akewo kuti: “Leronso ndinalota maloto ena. Ndinalota dzuwa ndi mwezi ndiponso nyenyezi zokwanira 11 zikundigwadira.”+