Genesis 44:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atafika, Yuda+ ndi abale ake analowa m’nyumba ya Yosefe. Anamupeza akanali m’nyumbamo, ndipo anagwada n’kumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+ Genesis 45:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Pitani kwa bambo anga msanga, ndipo mukawauze kuti, ‘Mwana wanu Yosefe wati: “Mulungu wandiika ine kukhala mbuye wa dziko lonse la Iguputo.+ Bwerani kuno kwa ine, musachedwe.
14 Atafika, Yuda+ ndi abale ake analowa m’nyumba ya Yosefe. Anamupeza akanali m’nyumbamo, ndipo anagwada n’kumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+
9 “Pitani kwa bambo anga msanga, ndipo mukawauze kuti, ‘Mwana wanu Yosefe wati: “Mulungu wandiika ine kukhala mbuye wa dziko lonse la Iguputo.+ Bwerani kuno kwa ine, musachedwe.