Genesis 45:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Bwererani kwa bambo anga msanga, ndipo mukawauze kuti, ‘Mwana wanu Yosefe wanena kuti: “Mulungu wandiika ine kukhala mbuye wa dziko lonse la Iguputo.+ Bwerani kuno kwa ine, musachedwe.+
9 Bwererani kwa bambo anga msanga, ndipo mukawauze kuti, ‘Mwana wanu Yosefe wanena kuti: “Mulungu wandiika ine kukhala mbuye wa dziko lonse la Iguputo.+ Bwerani kuno kwa ine, musachedwe.+