Genesis 45:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Pitani kwa bambo anga msanga, ndipo mukawauze kuti, ‘Mwana wanu Yosefe wati: “Mulungu wandiika ine kukhala mbuye wa dziko lonse la Iguputo.+ Bwerani kuno kwa ine, musachedwe.
9 “Pitani kwa bambo anga msanga, ndipo mukawauze kuti, ‘Mwana wanu Yosefe wati: “Mulungu wandiika ine kukhala mbuye wa dziko lonse la Iguputo.+ Bwerani kuno kwa ine, musachedwe.