Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 45:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Atafika, anauza bambo awo kuti: “Yosefe uja ali moyo! Ndiye woyang’anira dziko lonse la Iguputo!”+ Yakobo atamva zimenezo sizinam’khudze chifukwa sanazikhulupirire.+

  • Machitidwe 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 ndipo anamulanditsa m’masautso ake onse. Anamupatsanso chisomo ndi nzeru pamaso pa Farao mfumu ya Iguputo. Ndipo anamuika kuti ayang’anire Iguputo ndi nyumba yonse ya Farao.+

  • 1 Yohane 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Komanso ife taona+ ndipo tikuchitira umboni+ kuti Atate anatumiza Mwana wake kuti akhale Mpulumutsi wa dziko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena