Genesis 42:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Komabe bambo awo anati: “Zoti mwana wanga apite nanu, izo ndakana, chifukwa m’bale wake anafa, ndipo iye anatsala yekha.+ Ngati angakumane ndi tsoka n’kufa panjira, ndithu mudzatsitsira ku Manda+ imvi zanga ndi chisoni.” Genesis 44:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma mmodzi wa awiriwo anandisiya, ndipo ndinafuula kuti: “Kalanga ine! Ndithu wakhadzulidwa mwana wanga!”+ Mpaka lero sindinamuonenso. Luka 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma kwa iwo, zimene anali kuwauzazo zinali zopanda pake ndipo sanawakhulupirire amayiwo.+
38 Komabe bambo awo anati: “Zoti mwana wanga apite nanu, izo ndakana, chifukwa m’bale wake anafa, ndipo iye anatsala yekha.+ Ngati angakumane ndi tsoka n’kufa panjira, ndithu mudzatsitsira ku Manda+ imvi zanga ndi chisoni.”
28 Koma mmodzi wa awiriwo anandisiya, ndipo ndinafuula kuti: “Kalanga ine! Ndithu wakhadzulidwa mwana wanga!”+ Mpaka lero sindinamuonenso.