Genesis 45:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atafika, anauza bambo awo kuti: “Yosefe uja ali moyo! Ndiye woyang’anira dziko lonse la Iguputo!”+ Yakobo atamva zimenezo sizinam’khudze chifukwa sanazikhulupirire.+
26 Atafika, anauza bambo awo kuti: “Yosefe uja ali moyo! Ndiye woyang’anira dziko lonse la Iguputo!”+ Yakobo atamva zimenezo sizinam’khudze chifukwa sanazikhulupirire.+