Genesis 37:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Bambo awo anauyang’anitsitsa mkanjowo. Ndiyeno anafuula kuti: “Kalanga ine! Mkanjowu ndi wa mwana wanga! Chilombo cholusa chamudya basi mwana wanga.+ Wakhadzulidwa+ ndithu mwana wanga Yosefe!” Genesis 44:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ife tinakuyankhani mbuyanga kuti, ‘Bambo tili nawo koma ndi okalamba. Ali ndi mwana amene anabereka atakalamba, amene ndiye wamng’ono pa ife tonse.+ M’bale wake wa mimba imodzi anamwalira, moti anatsala yekha,+ ndipo bambo amam’konda kwambiri.’
33 Bambo awo anauyang’anitsitsa mkanjowo. Ndiyeno anafuula kuti: “Kalanga ine! Mkanjowu ndi wa mwana wanga! Chilombo cholusa chamudya basi mwana wanga.+ Wakhadzulidwa+ ndithu mwana wanga Yosefe!”
20 Ife tinakuyankhani mbuyanga kuti, ‘Bambo tili nawo koma ndi okalamba. Ali ndi mwana amene anabereka atakalamba, amene ndiye wamng’ono pa ife tonse.+ M’bale wake wa mimba imodzi anamwalira, moti anatsala yekha,+ ndipo bambo amam’konda kwambiri.’