Ekisodo 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngati nyamayo inaphedwa ndi chilombo,+ azibweretsa nyama yakufayo monga umboni.+ Asalipire pa nyama iliyonse yophedwa ndi chilombo. 2 Mafumu 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pomalizira pake Elisa anatembenuka ndipo anawaona. Atatero anawaitanira tsoka+ m’dzina la Yehova. Kenako zimbalangondo ziwiri zazikazi+ zinatuluka m’thengo n’kukhadzulapo anyamata 42.+
13 Ngati nyamayo inaphedwa ndi chilombo,+ azibweretsa nyama yakufayo monga umboni.+ Asalipire pa nyama iliyonse yophedwa ndi chilombo.
24 Pomalizira pake Elisa anatembenuka ndipo anawaona. Atatero anawaitanira tsoka+ m’dzina la Yehova. Kenako zimbalangondo ziwiri zazikazi+ zinatuluka m’thengo n’kukhadzulapo anyamata 42.+