Genesis 44:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma mmodzi wa awiriwo anandisiya, ndipo ndinafuula kuti: “Kalanga ine! Ndithu wakhadzulidwa mwana wanga!”+ Mpaka lero sindinamuonenso.
28 Koma mmodzi wa awiriwo anandisiya, ndipo ndinafuula kuti: “Kalanga ine! Ndithu wakhadzulidwa mwana wanga!”+ Mpaka lero sindinamuonenso.