Genesis 37:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Bambo awo anauyang’anitsitsa mkanjowo. Ndiyeno anafuula kuti: “Kalanga ine! Mkanjowu ndi wa mwana wanga! Chilombo cholusa chamudya basi mwana wanga.+ Wakhadzulidwa+ ndithu mwana wanga Yosefe!”
33 Bambo awo anauyang’anitsitsa mkanjowo. Ndiyeno anafuula kuti: “Kalanga ine! Mkanjowu ndi wa mwana wanga! Chilombo cholusa chamudya basi mwana wanga.+ Wakhadzulidwa+ ndithu mwana wanga Yosefe!”