Salimo 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndilangizeni, inu Yehova, kuti ndiyende m’njira yanu.+Nditsogolereni m’njira yowongoka kuti nditetezeke kwa adani anga. Salimo 86:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+Ndidzayenda m’choonadi chanu.+Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+ Yeremiya 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+
11 Ndilangizeni, inu Yehova, kuti ndiyende m’njira yanu.+Nditsogolereni m’njira yowongoka kuti nditetezeke kwa adani anga.
11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+Ndidzayenda m’choonadi chanu.+Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+
23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+