1 Samueli 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Samueli anapitiriza kukula ndipo Yehova anali naye,+ moti palibe mawu ake alionse amene anapita padera.+ Yobu 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Elihu anali ndi mawu koma anadikira kuti Yobu amalize, chifukwa anthuwo anali aakulu kwa Elihuyo.+ Mlaliki 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wosauka koma wanzeru ali bwino+ kuposa mfumu yokalamba koma yopusa,+ imene sionanso kufunika kochenjezedwa.+ Luka 2:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma onse amene anali kumumvetsera anadabwa kwambiri ndi mayankho ake komanso poona kuti anali womvetsa zinthu kwambiri.+
19 Samueli anapitiriza kukula ndipo Yehova anali naye,+ moti palibe mawu ake alionse amene anapita padera.+
13 Mwana wosauka koma wanzeru ali bwino+ kuposa mfumu yokalamba koma yopusa,+ imene sionanso kufunika kochenjezedwa.+
47 Koma onse amene anali kumumvetsera anadabwa kwambiri ndi mayankho ake komanso poona kuti anali womvetsa zinthu kwambiri.+