Numeri 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Akaziwo ankabwera kudzaitana Aisiraeliwo kuti azipita nawo limodzi kokapereka nsembe kwa milungu yawo.+ Kumeneko, Aisiraeliwo ankadya ndi kugwadira milungu ya Amowabuwo.+ 1 Mafumu 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene iye anali kukalamba,+ akazi ake anali atapotoza+ mtima wake moti iye anali kutsatira milungu ina.+ Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ monga mmene anachitira Davide bambo ake.
2 Akaziwo ankabwera kudzaitana Aisiraeliwo kuti azipita nawo limodzi kokapereka nsembe kwa milungu yawo.+ Kumeneko, Aisiraeliwo ankadya ndi kugwadira milungu ya Amowabuwo.+
4 Pamene iye anali kukalamba,+ akazi ake anali atapotoza+ mtima wake moti iye anali kutsatira milungu ina.+ Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ monga mmene anachitira Davide bambo ake.