Aheberi 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati wabwerera m’mbuyo, ine sindikondwera naye.”+ 2 Petulo 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndithudi, ngati anapulumuka ku zoipitsa za dzikoli+ mwa kumudziwa molondola Ambuye ndi Mpulumutsi Yesu Khristu, koma alowereranso m’zinthu zomwe zija ndi kugonjetsedwa nazo,+ potsirizira pake makhalidwe awo amakhala oipa kwambiri kuposa poyamba.+
38 “Koma wolungama wanga adzakhala ndi moyo mwa chikhulupiriro chake,”+ ndipo “ngati wabwerera m’mbuyo, ine sindikondwera naye.”+
20 Ndithudi, ngati anapulumuka ku zoipitsa za dzikoli+ mwa kumudziwa molondola Ambuye ndi Mpulumutsi Yesu Khristu, koma alowereranso m’zinthu zomwe zija ndi kugonjetsedwa nazo,+ potsirizira pake makhalidwe awo amakhala oipa kwambiri kuposa poyamba.+