Mateyu 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Poyankha Yesu anamuuza kuti: “Pa nthawi ino lola kuti zikhale choncho, chifukwa n’koyenera kwa ife kutero kuti tikwaniritse chilungamo chonse.”+ Atatero, anasiya kumuletsa. Mateyu 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pakuti Yohane anabwera kwa inu m’njira yachilungamo,+ koma inu simunam’khulupirire.+ Koma okhometsa msonkho ndi mahule anam’khulupirira,+ Ngakhale kuti inu munaona zimenezi, simunamve chisoni n’kusintha maganizo anu kuti mum’khulupirire.
15 Poyankha Yesu anamuuza kuti: “Pa nthawi ino lola kuti zikhale choncho, chifukwa n’koyenera kwa ife kutero kuti tikwaniritse chilungamo chonse.”+ Atatero, anasiya kumuletsa.
32 Pakuti Yohane anabwera kwa inu m’njira yachilungamo,+ koma inu simunam’khulupirire.+ Koma okhometsa msonkho ndi mahule anam’khulupirira,+ Ngakhale kuti inu munaona zimenezi, simunamve chisoni n’kusintha maganizo anu kuti mum’khulupirire.