Mateyu 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kodi ubatizo wa Yohane unachokera kuti? Kumwamba kapena kwa anthu?”+ Koma iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ atifunsa kuti, ‘Nanga n’chifukwa chiyani simunamukhulupirire?’+ Luka 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma Afarisi ndi anthu odziwa Chilamulo ananyalanyaza malangizo+ amene Mulungu anawapatsa. Choncho Yohane sanawabatize.)
25 Kodi ubatizo wa Yohane unachokera kuti? Kumwamba kapena kwa anthu?”+ Koma iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ atifunsa kuti, ‘Nanga n’chifukwa chiyani simunamukhulupirire?’+
30 Koma Afarisi ndi anthu odziwa Chilamulo ananyalanyaza malangizo+ amene Mulungu anawapatsa. Choncho Yohane sanawabatize.)