Mateyu 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pakuti Yohane anabwera kwa inu m’njira yachilungamo,+ koma inu simunam’khulupirire.+ Koma okhometsa msonkho ndi mahule anam’khulupirira,+ Ngakhale kuti inu munaona zimenezi, simunamve chisoni n’kusintha maganizo anu kuti mum’khulupirire. Maliko 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pamenepo iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ iye anena kuti, ‘Nanga n’chifukwa chiyani simunamukhulupirire?’+ Luka 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma Afarisi ndi anthu odziwa Chilamulo ananyalanyaza malangizo+ amene Mulungu anawapatsa. Choncho Yohane sanawabatize.)
32 Pakuti Yohane anabwera kwa inu m’njira yachilungamo,+ koma inu simunam’khulupirire.+ Koma okhometsa msonkho ndi mahule anam’khulupirira,+ Ngakhale kuti inu munaona zimenezi, simunamve chisoni n’kusintha maganizo anu kuti mum’khulupirire.
31 Pamenepo iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ iye anena kuti, ‘Nanga n’chifukwa chiyani simunamukhulupirire?’+
30 Koma Afarisi ndi anthu odziwa Chilamulo ananyalanyaza malangizo+ amene Mulungu anawapatsa. Choncho Yohane sanawabatize.)