-
1 Mbiri 21:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Davide anauza Mulungu woona kuti: “Kodi si ine amene ndinanena kuti awerenge anthu? Ine ndi amene ndachimwa, ineyo ndi amene ndalakwa.+ Nanga nkhosazi zalakwa chiyani? Chonde Yehova Mulungu wanga, dzanja lanu lindilange ineyo ndi anthu amʼnyumba ya bambo anga. Koma musagwetsere mliriwu anthu anu.”+
-