Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Koma ine ndidzabweretsa chigumula+ chamadzi padziko lapansi, kuti chiwononge chamoyo+ chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mphamvu ya moyo* m’thupi mwake. Chilichonse cha m’dziko lapansi chidzafa.+

  • Genesis 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Zamoyo zamtundu uliwonse, zokhala ndi mphamvu ya moyo+ m’thupi mwawo, zinali kupita ziwiriziwiri m’chingalawa mmene munali Nowa.

  • Yobu 27:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pamene mpweya wanga udakali wonse mwa ine,

      Ndiponso pamene mzimu wa Mulungu udakali m’mphuno mwanga,+

  • Mlaliki 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pakuti ana a anthu ali ndi mapeto, ndipo zinyamanso zili ndi mapeto. Mapeto a zonsezi ndi ofanana.+ Nyama imafa ndipo munthunso amafa.+ Mzimu wa zonsezi ndi umodzi,+ moti munthu saposa nyama, pakuti zonse n’zachabechabe.

  • Yesaya 42:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mulungu woona Yehova, amene analenga kumwamba+ ndiponso Wokutambasula Wamkulu,+ amene anakhazikitsa dziko lapansi+ ndi zonse zimene zili mmenemo,+ amene anapereka mpweya+ kwa anthu amene ali mmenemo,+ ndi mzimu kwa anthu amene amayenda padzikopo,+ iye wanena kuti:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena