Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chilichonse chokhala ndi mpweya wa moyo* m’mphuno mwake, kutanthauza zonse zimene zinali pamtunda, zinafa.+

  • Yobu 27:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Pamene mpweya wanga udakali wonse mwa ine,

      Ndiponso pamene mzimu wa Mulungu udakali m’mphuno mwanga,+

  • Yobu 33:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mzimu wa Mulungu unandiumba,+

      Mpweya wa Wamphamvuyonse unandipatsa moyo.+

  • Yesaya 42:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mulungu woona Yehova, amene analenga kumwamba+ ndiponso Wokutambasula Wamkulu,+ amene anakhazikitsa dziko lapansi+ ndi zonse zimene zili mmenemo,+ amene anapereka mpweya+ kwa anthu amene ali mmenemo,+ ndi mzimu kwa anthu amene amayenda padzikopo,+ iye wanena kuti:

  • Machitidwe 17:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Komanso satumikiridwa ndi manja a anthu ngati kuti amasowa kanthu,+ chifukwa ndi iyeyo amene amapatsa anthu onse moyo,+ mpweya,+ ndi zinthu zonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena