Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 104:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mukaphimba nkhope yanu, zimasokonezeka.+

      Mukachotsa mzimu wawo, zimafa,+

      Ndipo zimabwerera kufumbi.+

  • Yesaya 53:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa chifukwa chimenechi, ndidzamupatsa gawo pamodzi ndi ambiri+ ndipo iye adzagawana zolanda ndi amphamvu,+ chifukwa anakhuthula moyo wake mu imfa+ ndipo anaonedwa monga mmodzi wa ochimwa.+ Iye ananyamula tchimo la anthu ambiri+ ndipo analowererapo kuti athandize olakwa.+

  • Mateyu 27:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Pamenepo Yesu anafuulanso mokweza mawu, kenako anatsirizika.+

  • Maliko 15:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ndiyeno Yesu anafuula mokweza mawu, ndipo anatsirizika.+

  • Luka 23:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Pamenepo Yesu anafuula mokweza mawu kuti: “Atate, ndikuikiza mzimu*+ wanga m’manja mwanu.” Atanena zimenezi anatsirizika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena