Salimo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndathiridwa pansi ngati madzi.+Mafupa anga onse alekanalekana.+Mtima wanga wakhala ngati phula,+Wasungunuka mkati mwanga.+ Mateyu 26:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Vinyoyu akuimira+ ‘magazi+ anga a pangano,’+ amene adzakhetsedwa chifukwa cha anthu ambiri+ kuti machimo akhululukidwe.+ Aheberi 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero, popeza kuti “ana” amenewo onse ndi amagazi ndi mnofu, iyenso anakhala wamagazi ndi mnofu.+ Anachita izi kuti kudzera mu imfa yake,+ awononge+ Mdyerekezi,+ amene ali ndi njira yobweretsera imfa.+ 1 Petulo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma munamasulidwa ndi magazi amtengo wapatali,+ monga a nkhosa yopanda chilema ndi yopanda mawanga,+ magazi a Khristu.+
14 Ndathiridwa pansi ngati madzi.+Mafupa anga onse alekanalekana.+Mtima wanga wakhala ngati phula,+Wasungunuka mkati mwanga.+
28 Vinyoyu akuimira+ ‘magazi+ anga a pangano,’+ amene adzakhetsedwa chifukwa cha anthu ambiri+ kuti machimo akhululukidwe.+
14 Chotero, popeza kuti “ana” amenewo onse ndi amagazi ndi mnofu, iyenso anakhala wamagazi ndi mnofu.+ Anachita izi kuti kudzera mu imfa yake,+ awononge+ Mdyerekezi,+ amene ali ndi njira yobweretsera imfa.+
19 Koma munamasulidwa ndi magazi amtengo wapatali,+ monga a nkhosa yopanda chilema ndi yopanda mawanga,+ magazi a Khristu.+